2 Mafumu 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Bwerera, kauze Hezekiya mtsogoleri+ wa anthu anga kuti, ‘Yehova Mulungu+ wa Davide kholo lako wanena kuti: “Ndamva+ pemphero lako,+ ndipo ndaona misozi yako.+ Ndikuchiritsa.+ Pa tsiku lachitatu udzapita kunyumba ya Yehova.+ Salimo 39:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Imvani pemphero langa, inu Yehova,Ndipo tcherani khutu pamene ndikufuula kupempha thandizo.+Musandinyalanyaze pamene ndikugwetsa misozi.+Pakuti ndine mlendo wanu,+Mlendo wokhala nanu monga anachitira makolo anga onse.+ Salimo 56:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu mwalemba za kuthawathawa kwanga.+Sungani misozi yanga m’thumba lanu lachikopa.+Kodi misozi yanga sili m’buku lanu?+
5 “Bwerera, kauze Hezekiya mtsogoleri+ wa anthu anga kuti, ‘Yehova Mulungu+ wa Davide kholo lako wanena kuti: “Ndamva+ pemphero lako,+ ndipo ndaona misozi yako.+ Ndikuchiritsa.+ Pa tsiku lachitatu udzapita kunyumba ya Yehova.+
12 Imvani pemphero langa, inu Yehova,Ndipo tcherani khutu pamene ndikufuula kupempha thandizo.+Musandinyalanyaze pamene ndikugwetsa misozi.+Pakuti ndine mlendo wanu,+Mlendo wokhala nanu monga anachitira makolo anga onse.+
8 Inu mwalemba za kuthawathawa kwanga.+Sungani misozi yanga m’thumba lanu lachikopa.+Kodi misozi yanga sili m’buku lanu?+