Yesaya 3:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Amuna ako adzaphedwa ndi lupanga, ndipo anthu ako amphamvu adzaphedwa pa nkhondo.+