Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 49:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Koma uta wake unakhalabe pamalo ake achikhalire,+ ndipo manja ake anali amphamvu ndi ochenjera.+ M’busayo, Mwala wa Isiraeli,+ akuchokera m’manja mwa Wamphamvu wa Yakobo.+ M’busayo akuchokera kumeneko ndithu.

  • Yesaya 49:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Iwo sadzakhala ndi njala+ ndipo sadzamva ludzu.+ Sadzamva kutentha kapena kupsa ndi dzuwa.+ Pakuti yemwe amawamvera chisoni adzawatsogolera+ ndipo adzapita nawo ku akasupe amadzi.+

  • Aheberi 13:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tsopano, Mulungu wamtendere,+ amene anaukitsa kwa akufa+ m’busa wamkulu+ wa nkhosa+ wokhala ndi magazi a pangano losatha,+ Ambuye wathu Yesu,

  • 1 Petulo 2:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pakuti munali ngati nkhosa zosochera,+ koma tsopano mwabwerera kwa m’busa+ wanu ndi woyang’anira miyoyo yanu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena