Yesaya 40:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kodi anthu inu simukudziwa? Kodi simunamve? Kodi simunauzidwe kuyambira pa chiyambi? Kodi simunamvetsetse umboni umene wakhalapo kuyambira pamene dziko lapansi linakhalapo?+
21 Kodi anthu inu simukudziwa? Kodi simunamve? Kodi simunauzidwe kuyambira pa chiyambi? Kodi simunamvetsetse umboni umene wakhalapo kuyambira pamene dziko lapansi linakhalapo?+