Salimo 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Patsala kanthawi kochepa, woipa sadzakhalakonso.+Udzayang’ana pamene anali kukhala, ndipo sadzapezekapo.+ Salimo 37:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Koma anafa ndipo sanapezekenso.+Ndinamufunafuna ndipo sindinamupeze.+
10 Patsala kanthawi kochepa, woipa sadzakhalakonso.+Udzayang’ana pamene anali kukhala, ndipo sadzapezekapo.+