2 Mbiri 26:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nkhani zina zokhudza Uziya,+ zoyambirira ndi zomalizira, zinalembedwa ndi mneneri Yesaya+ mwana wa Amozi.+ Yesaya 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’chaka chimene Mfumu Uziya inamwalira,+ ine ndinaona Yehova+ atakhala pampando wachifumu+ wolemekezeka umene unali pamalo okwezeka, ndipo zovala zake zinadzaza m’kachisi.+
22 Nkhani zina zokhudza Uziya,+ zoyambirira ndi zomalizira, zinalembedwa ndi mneneri Yesaya+ mwana wa Amozi.+
6 M’chaka chimene Mfumu Uziya inamwalira,+ ine ndinaona Yehova+ atakhala pampando wachifumu+ wolemekezeka umene unali pamalo okwezeka, ndipo zovala zake zinadzaza m’kachisi.+