Yeremiya 44:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako Yehova sanathenso kupirira zimenezo chifukwa zochita zanu zinaipa kwambiri, chifukwa munachita zinthu zonyansa.+ Chotero dziko lanu linasanduka bwinja, chinthu chodabwitsa ndi chotembereredwa ndipo tsopano mulibe munthu wokhalamo.+
22 Kenako Yehova sanathenso kupirira zimenezo chifukwa zochita zanu zinaipa kwambiri, chifukwa munachita zinthu zonyansa.+ Chotero dziko lanu linasanduka bwinja, chinthu chodabwitsa ndi chotembereredwa ndipo tsopano mulibe munthu wokhalamo.+