Salimo 50:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu wathu adzabwera ndipo sadzakhala chete.+Pamaso pake pali moto wonyeketsa,+Ndipo pamalo onse omuzungulira pali mkuntho wamphamvu.+ Salimo 83:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 83 Inu Mulungu, musakhale chete.+Musakhale phee osalankhulapo kanthu ndipo musakhale duu osachitapo kanthu, inu Mulungu.+
3 Mulungu wathu adzabwera ndipo sadzakhala chete.+Pamaso pake pali moto wonyeketsa,+Ndipo pamalo onse omuzungulira pali mkuntho wamphamvu.+
83 Inu Mulungu, musakhale chete.+Musakhale phee osalankhulapo kanthu ndipo musakhale duu osachitapo kanthu, inu Mulungu.+