Yesaya 40:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu amasankha mtengo wosawola kuti ukhale ngati chopereka.+ Amafunafuna mmisiri waluso kuti amupangire chifaniziro chosema+ chimene sichingagwedezeke.+ Yeremiya 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Miyambo ya anthu amenewa+ ndi yopanda pake, chifukwa mmisiri amagwetsa mtengo+ m’nkhalango ndi kusema fano pogwiritsa ntchito sompho.+
20 Munthu amasankha mtengo wosawola kuti ukhale ngati chopereka.+ Amafunafuna mmisiri waluso kuti amupangire chifaniziro chosema+ chimene sichingagwedezeke.+
3 Miyambo ya anthu amenewa+ ndi yopanda pake, chifukwa mmisiri amagwetsa mtengo+ m’nkhalango ndi kusema fano pogwiritsa ntchito sompho.+