Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 44:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pali munthu amene ntchito yake ndi yogwetsa mitengo ya mkungudza. Iye amasankha mtengo wamtundu winawake, waukulu kwambiri, n’kuusiya kuti ukule n’kukhwima pakati pa mitengo ya m’nkhalango.+ Iye anabzala mtengo wa paini, ndipo mvula yaukulitsa kwambiri.

  • Yesaya 45:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Sonkhanani pamodzi n’kubwera kwa ine.+ Unjikanani pamodzi, inu anthu opulumuka ku mitundu ya anthu.+ Amene amanyamula chifaniziro chawo chosema chamtengo sadziwa kanthu, mofanana ndi amene amapemphera kwa mulungu woti sangawapulumutse.+

  • Habakuku 2:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Kodi chifaniziro chosema, chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula ndiponso mphunzitsi wonama,+ zili ndi phindu lanji+ kuti wozipanga azizikhulupirira+ ndipo azipanga milungu yopanda pake yosalankhula?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena