Salimo 72:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Adzatsika ngati mvula pa udzu umene wadulidwa,+Ngati mvula yambiri yamvumbi imene imanyowetsa kwambiri nthaka.+ Ezekieli 34:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Nkhosazo komanso malo ozungulira phiri langa ndidzawasandutsa dalitso.+ Ndidzagwetsa mvula yambiri pa nthawi yake. Kudzagwa mvula yambiri yamadalitso.+
6 Adzatsika ngati mvula pa udzu umene wadulidwa,+Ngati mvula yambiri yamvumbi imene imanyowetsa kwambiri nthaka.+
26 Nkhosazo komanso malo ozungulira phiri langa ndidzawasandutsa dalitso.+ Ndidzagwetsa mvula yambiri pa nthawi yake. Kudzagwa mvula yambiri yamadalitso.+