Salimo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mitunduyo udzaiswa ndi ndodo yachifumu yachitsulo,+Udzaiphwanya ngati mbiya yadothi, n’kukhala zidutswazidutswa.”+ 1 Akorinto 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kapena “kodi tikufuna kuputa nsanje+ ya Yehova”? Kodi mphamvu zathu zingafanane ndi zake?+
9 Mitunduyo udzaiswa ndi ndodo yachifumu yachitsulo,+Udzaiphwanya ngati mbiya yadothi, n’kukhala zidutswazidutswa.”+