Yesaya 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsoka kwa amene amadziona ngati anzeru komanso amadziyesa ochenjera.+ Aroma 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ngakhale anali kunena motsimikiza kuti ndi anzeru, iwo anakhala opusa+