Miyambo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Usamadzione kuti ndiwe wanzeru.+ Uziopa Yehova ndi kupatuka pa choipa.+ Miyambo 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu wonyoza amadana ndi munthu amene akum’dzudzula.+ Iye sadzapita kwa anthu anzeru.+ Yohane 9:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Yesu anati: “Mukanakhala akhungu, simukanakhala ndi tchimo. Koma popeza mukunena kuti, ‘Tikuona.’+ Tchimo+ lanu likhalabe chikhalire.” Aroma 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ngakhale anali kunena motsimikiza kuti ndi anzeru, iwo anakhala opusa+ Aroma 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muziona ena mmene inuyo mumadzionera.+ Musamaganize modzikweza,+ koma khalani ndi mtima wodzichepetsa.+ Musadziyese anzeru.+
41 Yesu anati: “Mukanakhala akhungu, simukanakhala ndi tchimo. Koma popeza mukunena kuti, ‘Tikuona.’+ Tchimo+ lanu likhalabe chikhalire.”
16 Muziona ena mmene inuyo mumadzionera.+ Musamaganize modzikweza,+ koma khalani ndi mtima wodzichepetsa.+ Musadziyese anzeru.+