Salimo 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Sonyezani kukoma mtima kosatha mwa kuchita zodabwitsa,+ inu Mpulumutsi wa anthu othawira kwa inu,Amene akuthawa anthu ogalukira dzanja lanu lamanja.+ 1 Timoteyo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Paulo, mtumwi+ wa Khristu Yesu molamulidwa ndi Mulungu+ Mpulumutsi wathu,+ ndi Khristu Yesu yemwe ali chiyembekezo chathu,+
7 Sonyezani kukoma mtima kosatha mwa kuchita zodabwitsa,+ inu Mpulumutsi wa anthu othawira kwa inu,Amene akuthawa anthu ogalukira dzanja lanu lamanja.+
1 Ine Paulo, mtumwi+ wa Khristu Yesu molamulidwa ndi Mulungu+ Mpulumutsi wathu,+ ndi Khristu Yesu yemwe ali chiyembekezo chathu,+