Salimo 102:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Zimenezi zidzatha, koma inu mudzakhalapobe.+Ndipo zonsezi zidzatha ngati chovala.+Mofanana ndi zovala zimene zatha, mudzapezerapo zina ndipo nazonso zidzatha.+
26 Zimenezi zidzatha, koma inu mudzakhalapobe.+Ndipo zonsezi zidzatha ngati chovala.+Mofanana ndi zovala zimene zatha, mudzapezerapo zina ndipo nazonso zidzatha.+