Salimo 94:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti zigamulo zidzayambiranso kukhala zachilungamo,+Ndipo onse owongoka mtima adzazitsatira. Miyambo 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amene akufunafuna chilungamo+ ndiponso kukoma mtima kosatha adzapeza moyo, chilungamo ndi ulemerero.+ Zefaniya 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 bwerani kwa Yehova,+ inu nonse ofatsa a padziko lapansi,+ amene mwakhala mukutsatira zigamulo zake. Yesetsani kukhala olungama,+ yesetsani kukhala ofatsa.+ Mwina+ mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+ Mateyu 6:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Chotero pitirizani kufunafuna ufumu choyamba ndi chilungamo chake,+ ndipo zina zonsezi zidzawonjezedwa kwa inu.+ 1 Timoteyo 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma munthu wa Mulungu iwe, thawa zinthu zimenezi.+ M’malomwake tsatira chilungamo, kudzipereka kwa Mulungu, chikhulupiriro, chikondi, chipiriro, ndi kufatsa.+
21 Amene akufunafuna chilungamo+ ndiponso kukoma mtima kosatha adzapeza moyo, chilungamo ndi ulemerero.+
3 bwerani kwa Yehova,+ inu nonse ofatsa a padziko lapansi,+ amene mwakhala mukutsatira zigamulo zake. Yesetsani kukhala olungama,+ yesetsani kukhala ofatsa.+ Mwina+ mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+
33 “Chotero pitirizani kufunafuna ufumu choyamba ndi chilungamo chake,+ ndipo zina zonsezi zidzawonjezedwa kwa inu.+
11 Koma munthu wa Mulungu iwe, thawa zinthu zimenezi.+ M’malomwake tsatira chilungamo, kudzipereka kwa Mulungu, chikhulupiriro, chikondi, chipiriro, ndi kufatsa.+