Luka 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho anaitana kuti, ‘Atate Abulahamu,+ ndichitireni chifundo. Mutume Lazaro kuti aviike nsonga ya chala chake m’madzi kuti aziziritse lilime langa,+ chifukwa ndikuzunzika m’moto wolilimawu.’+
24 Choncho anaitana kuti, ‘Atate Abulahamu,+ ndichitireni chifundo. Mutume Lazaro kuti aviike nsonga ya chala chake m’madzi kuti aziziritse lilime langa,+ chifukwa ndikuzunzika m’moto wolilimawu.’+