Yesaya 51:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yang’anani kwa tate+ wanu Abulahamu,+ ndi kwa Sara+ amene anakuberekani ndi zowawa za pobereka. Abulahamuyo anali munthu mmodzi pamene ndinamuitana,+ koma ndinamudalitsa ndi kumusandutsa anthu ambiri.+ Mateyu 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musamadzinyenge kuti, ‘Tili ndi atate wathu Abulahamu.’+ Pakuti ndikukuuzani kuti Mulungu angathe kuutsira Abulahamu+ ana kuchokera kumiyala iyi.
2 Yang’anani kwa tate+ wanu Abulahamu,+ ndi kwa Sara+ amene anakuberekani ndi zowawa za pobereka. Abulahamuyo anali munthu mmodzi pamene ndinamuitana,+ koma ndinamudalitsa ndi kumusandutsa anthu ambiri.+
9 Musamadzinyenge kuti, ‘Tili ndi atate wathu Abulahamu.’+ Pakuti ndikukuuzani kuti Mulungu angathe kuutsira Abulahamu+ ana kuchokera kumiyala iyi.