Deuteronomo 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti mawu a chilamulowo ali pafupi kwambiri ndi iwe, ali m’kamwa mwako ndi mumtima mwako+ kuti uwatsatire.+ Yesaya 46:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ine ndabweretsa pafupi chilungamo changa.+ Chilungamocho sichili kutali,+ ndipo chipulumutso changa sichidzachedwa.+ Ndidzapereka chipulumutso mu Ziyoni, ndipo Isiraeli ndidzam’patsa kukongola kwanga.”+
14 Pakuti mawu a chilamulowo ali pafupi kwambiri ndi iwe, ali m’kamwa mwako ndi mumtima mwako+ kuti uwatsatire.+
13 Ine ndabweretsa pafupi chilungamo changa.+ Chilungamocho sichili kutali,+ ndipo chipulumutso changa sichidzachedwa.+ Ndidzapereka chipulumutso mu Ziyoni, ndipo Isiraeli ndidzam’patsa kukongola kwanga.”+