-
Salimo 8:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndikayang’ana kumwamba, ntchito ya zala zanu,+
Mwezi ndi nyenyezi zimene munapanga,+
-
Yesaya 40:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 “Kwezani maso anu kumwamba muone. Kodi ndani amene analenga zinthu zimenezo?+ Ndi amene akutsogolera gulu lonse la nyenyezizo malinga ndi chiwerengero chake, ndipo amaziitana potchula iliyonse dzina lake.+ Chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake zoopsa,+ ndiponso chifukwa chakuti ali ndi mphamvu zambiri zochitira zinthu, palibe imene imasowa.
-
-
-