Salimo 88:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mafunde a mkwiyo wanu woyaka moto andimiza.+Zinthu zochititsa mantha zochokera kwa inu zandisowetsa chonena.+ Yesaya 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chifukwa cha mkwiyo wa Yehova wa makamu, dzikolo layaka moto ndipo anthu adzakhala ngati chakudya cha motowo.+ Palibe amene adzamvere chisoni aliyense, ngakhale m’bale wake.+ Chivumbulutso 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 adzamwanso vinyo wosasungunula wa mkwiyo+ wa Mulungu amene akuthiridwa m’kapu ya mkwiyo wake. Ndipo adzazunzidwa+ ndi moto ndi sulufule+ pamaso pa angelo oyera, ndi pamaso pa Mwanawankhosa.
16 Mafunde a mkwiyo wanu woyaka moto andimiza.+Zinthu zochititsa mantha zochokera kwa inu zandisowetsa chonena.+
19 Chifukwa cha mkwiyo wa Yehova wa makamu, dzikolo layaka moto ndipo anthu adzakhala ngati chakudya cha motowo.+ Palibe amene adzamvere chisoni aliyense, ngakhale m’bale wake.+
10 adzamwanso vinyo wosasungunula wa mkwiyo+ wa Mulungu amene akuthiridwa m’kapu ya mkwiyo wake. Ndipo adzazunzidwa+ ndi moto ndi sulufule+ pamaso pa angelo oyera, ndi pamaso pa Mwanawankhosa.