Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 75:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 M’dzanja la Yehova muli kapu.+

      Kapuyo yadzaza ndi vinyo wosakaniza ndi zokometsera ndipo akuchita thovu.

      Ndithudi, iye adzatsanula vinyo yense amene ali m’kapuyo kuphatikizapo nsenga zake.

      Anthu onse oipa padziko lapansi adzamwa ndi kugugudiza nsengazo.”+

  • Chivumbulutso 11:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma mitundu ya anthu inakwiya, ndipo mkwiyo wanu unafika. Inafikanso nthawi yoikidwiratu yakuti akufa aweruzidwe, nthawi yopereka mphoto+ kwa akapolo anu aneneri,+ ndiponso kwa oyerawo, ndi oopa dzina lanu, olemekezeka ndi onyozeka omwe.+ Komanso, nthawi yowononga+ amene akuwononga dziko lapansi.”+

  • Chivumbulutso 16:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Pamenepo mzinda waukulu+ unagawika zigawo zitatu, ndipo mizinda ya mitundu ya anthu inagwa. Ndiyeno Mulungu anakumbukira Babulo Wamkulu,+ kuti amupatse kapu yokhala ndi vinyo wa mkwiyo wake waukulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena