Ekisodo 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako oyang’anira ntchito+ a Farao anamenya+ akapitawo a ana a Isiraeli amene iwo anawaika, n’kumati: “N’chifukwa chiyani dzulo ndi lero simunamalize kuumba njerwa+ zimene munauzidwa ngati mmene munali kuchitira kale?”+ Salimo 137:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kumeneko, amene anatigwira ukapolo anatiuza kuti tiwaimbire nyimbo,+Ndipo otinyozawo anatipempha kuti tiwasangalatse.+ Iwo anati:“Tiimbireni imodzi mwa nyimbo za ku Ziyoni.”+ Yeremiya 50:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Isiraeli ndi nkhosa yosochera.+ Mikango ndi imene yamuchititsa kuthawa.+ Poyamba, mfumu ya Asuri inadya Isiraeli,+ ndipo ulendo uno Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo yakukuta mafupa ake.+
14 Kenako oyang’anira ntchito+ a Farao anamenya+ akapitawo a ana a Isiraeli amene iwo anawaika, n’kumati: “N’chifukwa chiyani dzulo ndi lero simunamalize kuumba njerwa+ zimene munauzidwa ngati mmene munali kuchitira kale?”+
3 Kumeneko, amene anatigwira ukapolo anatiuza kuti tiwaimbire nyimbo,+Ndipo otinyozawo anatipempha kuti tiwasangalatse.+ Iwo anati:“Tiimbireni imodzi mwa nyimbo za ku Ziyoni.”+
17 “Isiraeli ndi nkhosa yosochera.+ Mikango ndi imene yamuchititsa kuthawa.+ Poyamba, mfumu ya Asuri inadya Isiraeli,+ ndipo ulendo uno Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo yakukuta mafupa ake.+