Luka 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Ulemerero kwa Mulungu kumwambamwamba,+ ndipo pansi pano mtendere+ pakati pa anthu amene iye amakondwera nawo.”+ Machitidwe 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komabe, amene anabalalitsidwa aja anapita m’zigawozo akulengeza uthenga wabwino wa mawu opatulika.+ Machitidwe 10:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mulungu anatumiza mawu+ kwa ana a Isiraeli ndi kulengeza kwa iwo uthenga wabwino wa mtendere+ kudzera mwa Yesu Khristu. Ameneyu ndiye Ambuye wa ena onse.+ Agalatiya 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno, Malemba ataoneratu kuti Mulungu adzayesa anthu a mitundu ina kukhala olungama chifukwa cha chikhulupiriro, analengezeratu uthenga wabwino kwa Abulahamu, kuti: “Kudzera mwa iwe, mitundu yonse idzadalitsidwa.”+ Aefeso 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chotero iye anabwera n’kulengeza uthenga wabwino wa mtendere+ kwa inuyo, inu akutali, ndipo analengezanso mtendere kwa apafupi,+
14 “Ulemerero kwa Mulungu kumwambamwamba,+ ndipo pansi pano mtendere+ pakati pa anthu amene iye amakondwera nawo.”+
4 Komabe, amene anabalalitsidwa aja anapita m’zigawozo akulengeza uthenga wabwino wa mawu opatulika.+
36 Mulungu anatumiza mawu+ kwa ana a Isiraeli ndi kulengeza kwa iwo uthenga wabwino wa mtendere+ kudzera mwa Yesu Khristu. Ameneyu ndiye Ambuye wa ena onse.+
8 Ndiyeno, Malemba ataoneratu kuti Mulungu adzayesa anthu a mitundu ina kukhala olungama chifukwa cha chikhulupiriro, analengezeratu uthenga wabwino kwa Abulahamu, kuti: “Kudzera mwa iwe, mitundu yonse idzadalitsidwa.”+
17 Chotero iye anabwera n’kulengeza uthenga wabwino wa mtendere+ kwa inuyo, inu akutali, ndipo analengezanso mtendere kwa apafupi,+