Yesaya 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo adzafuula mosangalala. Adzafuula mokondwa ali kunyanja, chifukwa cha kukwezeka kwa Yehova.+ Yesaya 62:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwe Yerusalemu, ine ndaika alonda pamakoma a mpanda wako.+ Nthawi zonse, tsiku lonse lathunthu ndi usiku wonse wathunthu, iwo asakhale chete.+ “Inu amene mukutchula dzina la Yehova,+ musakhale chete.+
6 Iwe Yerusalemu, ine ndaika alonda pamakoma a mpanda wako.+ Nthawi zonse, tsiku lonse lathunthu ndi usiku wonse wathunthu, iwo asakhale chete.+ “Inu amene mukutchula dzina la Yehova,+ musakhale chete.+