Yobu 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngakhale mtengo umakhala ndi chiyembekezo.Ukadulidwa umaphukanso,+Ndipo nthambi yake idzakhalapo mpaka kalekale. Yesaya 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nthambi+ idzatuluka pachitsa cha Jese,+ ndipo mphukira+ yotuluka pamizu yake idzakhala yobereka zipatso.+ Zekariya 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno udzamuuze kuti,“‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Munthu uyu+ dzina lake ndi Mphukira.+ Adzaphuka pamalo ake ndipo adzamanga kachisi wa Yehova.+ Afilipi 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Sanatero ayi, koma anasiya zonse zimene anali nazo n’kukhala ngati kapolo,+ ndi kukhala wofanana ndi anthu.+
7 Ngakhale mtengo umakhala ndi chiyembekezo.Ukadulidwa umaphukanso,+Ndipo nthambi yake idzakhalapo mpaka kalekale.
11 Nthambi+ idzatuluka pachitsa cha Jese,+ ndipo mphukira+ yotuluka pamizu yake idzakhala yobereka zipatso.+
12 Ndiyeno udzamuuze kuti,“‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Munthu uyu+ dzina lake ndi Mphukira.+ Adzaphuka pamalo ake ndipo adzamanga kachisi wa Yehova.+
7 Sanatero ayi, koma anasiya zonse zimene anali nazo n’kukhala ngati kapolo,+ ndi kukhala wofanana ndi anthu.+