2 Akorinto 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Utumiki wake ndi woti tilengeze kuti Mulungu anali kugwirizanitsa dziko+ ndi iyeyo+ kudzera mwa Khristu,+ moti sanawawerengere anthuwo machimo awo,+ ndipo watipatsa ifeyo ntchito yolengeza uthenga+ umenewu wokhazikitsanso mtendere.+ Akolose 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kuti kudzera mwa mwana wakeyo iye agwirizanitsenso+ zinthu zina zonse ndi iyeyo,+ pokhazikitsa mtendere+ mwa magazi+ amene iye anakhetsa pamtengo wozunzikirapo,*+ kaya zikhale zinthu zapadziko lapansi kapena zinthu zakumwamba.
19 Utumiki wake ndi woti tilengeze kuti Mulungu anali kugwirizanitsa dziko+ ndi iyeyo+ kudzera mwa Khristu,+ moti sanawawerengere anthuwo machimo awo,+ ndipo watipatsa ifeyo ntchito yolengeza uthenga+ umenewu wokhazikitsanso mtendere.+
20 Kuti kudzera mwa mwana wakeyo iye agwirizanitsenso+ zinthu zina zonse ndi iyeyo,+ pokhazikitsa mtendere+ mwa magazi+ amene iye anakhetsa pamtengo wozunzikirapo,*+ kaya zikhale zinthu zapadziko lapansi kapena zinthu zakumwamba.