Mateyu 27:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma iye anangokhala duu, osanena kanthu, moti bwanamkubwayo anadabwa kwambiri.+ Machitidwe 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndime ya m’Malemba imene anali kuwerenga mokwezayo, mawu ake ndi awa: “Iye anamutengera kokamupha ngati nkhosa. Ngati mwana wa nkhosa wongokhala chete pamene akumumeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+
32 Ndime ya m’Malemba imene anali kuwerenga mokwezayo, mawu ake ndi awa: “Iye anamutengera kokamupha ngati nkhosa. Ngati mwana wa nkhosa wongokhala chete pamene akumumeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+