Salimo 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Agalu andizungulira.+Khamu la anthu ochita zoipa landizinga.+Iwo akuluma manja ndi mapazi anga ngati mkango.+ Mateyu 26:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Pamenepo mkulu wa ansembe anang’amba malaya ake akunja n’kunena kuti: “Wanyoza Mulungu!+ Nanga n’kufunanso mboni zina pamenepa?+ Pano mwadzimvera nokha mmene akunyozera Mulungu.+ Yohane 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ayudawo anamuyankha kuti: “Tili ndi chilamulo ife,+ ndipo malinga ndi chilamulocho iyeyu ayenera kufa, chifukwa akudziyesa mwana wa Mulungu.”+
16 Agalu andizungulira.+Khamu la anthu ochita zoipa landizinga.+Iwo akuluma manja ndi mapazi anga ngati mkango.+
65 Pamenepo mkulu wa ansembe anang’amba malaya ake akunja n’kunena kuti: “Wanyoza Mulungu!+ Nanga n’kufunanso mboni zina pamenepa?+ Pano mwadzimvera nokha mmene akunyozera Mulungu.+
7 Ayudawo anamuyankha kuti: “Tili ndi chilamulo ife,+ ndipo malinga ndi chilamulocho iyeyu ayenera kufa, chifukwa akudziyesa mwana wa Mulungu.”+