Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Buku la mzere wa makolo+ a Yesu Khristu, mwana wa Davide,+ mwana wa Abulahamu:+

  • Luka 3:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pamene Yesu anayamba ntchito yake,+ anali ndi zaka pafupifupi 30.+ Anthu ankakhulupirira kuti Yesu anali

      mwana+ wa Yosefe,+

      mwana wa Heli,

  • Machitidwe 8:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Pamene anali kumuchitira zinthu zochititsa manyazi, anamuchotsera chiweruzo chomuyenera.+ Ndani angafotokoze tsatanetsatane wa mibadwo ya makolo ake? Chifukwa moyo wake wachotsedwa padziko lapansi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena