Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 11:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kunabwera Mwana wa munthu ndipo anali kudya ndi kumwa,+ koma anthu akunenabe kuti, ‘Taonani! Munthu wosusuka ndi wokonda kwambiri vinyo, bwenzi la okhometsa msonkho ndi ochimwa.’+ Mulimonsemo, nzeru imatsimikizirika kuti ndi yolungama chifukwa cha ntchito zake.”+

  • Maliko 15:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Komanso iwo anapachika achifwamba awiri limodzi ndi iye. Mmodzi anamupachika kudzanja lake lamanja, wina kumanzere kwake.+

  • Luka 22:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Pakuti ndikukuuzani kuti mawu olembedwawa ayenera kukwaniritsidwa mwa ine. Mawuwo ndi akuti, ‘Ndipo anamutenga ngati mmodzi wa anthu osamvera malamulo.’+ Pakuti chimene chikukhudza ine chikukwaniritsidwa.”+

  • Luka 23:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Anthuwo anatenganso amuna ena awiri ochita zoipa, kuti akawaphe limodzi ndi Yesu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena