Luka 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Afarisi ndi alembi awo ataona izi, anayamba kung’ung’udza ndi kufunsa ophunzira ake kuti: “N’chifukwa chiyani inu mumadya ndi kumwa limodzi ndi okhometsa msonkho ndi anthu ochimwa?”+ Luka 7:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kunabwera Mwana wa munthu ndipo iye akudya ndi kumwa, koma inu mumati, ‘Taonani! Munthu wosusuka ndi wokonda kwambiri vinyo, bwenzi la okhometsa msonkho ndi ochimwa!’+ Luka 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Afarisi ndi alembi ataona zimenezi anayamba kung’ung’udza kuti: “Munthu uyu amalandira anthu ochimwa ndi kudya nawo limodzi.”+ Luka 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma anthu ataona Yesu akulowa m’nyumbamo, onse anayamba kung’ung’udza,+ kuti: “Akupita kukakhala ndi munthu wochimwa.”
30 Afarisi ndi alembi awo ataona izi, anayamba kung’ung’udza ndi kufunsa ophunzira ake kuti: “N’chifukwa chiyani inu mumadya ndi kumwa limodzi ndi okhometsa msonkho ndi anthu ochimwa?”+
34 Kunabwera Mwana wa munthu ndipo iye akudya ndi kumwa, koma inu mumati, ‘Taonani! Munthu wosusuka ndi wokonda kwambiri vinyo, bwenzi la okhometsa msonkho ndi ochimwa!’+
2 Afarisi ndi alembi ataona zimenezi anayamba kung’ung’udza kuti: “Munthu uyu amalandira anthu ochimwa ndi kudya nawo limodzi.”+
7 Koma anthu ataona Yesu akulowa m’nyumbamo, onse anayamba kung’ung’udza,+ kuti: “Akupita kukakhala ndi munthu wochimwa.”