Yesaya 52:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Dzuka pafumbi pamene ulipo.+ Sansa fumbilo, khala pamalo aulemu iwe Yerusalemu. Masula zingwe zimene zili m’khosi mwako, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni wogwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.+ Chivumbulutso 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno ndidzachititsa mboni zanga ziwiri+ kunenera+ kwa masiku 1,260, zitavala ziguduli.”+
2 Dzuka pafumbi pamene ulipo.+ Sansa fumbilo, khala pamalo aulemu iwe Yerusalemu. Masula zingwe zimene zili m’khosi mwako, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni wogwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.+