Salimo 91:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzakutchinjiriza ndi mapiko ake,+Udzathawira pansi pa mapiko ake.+Choonadi chake+ chidzakhala chishango chako+ chachikulu ndi malo ako achitetezo. Yeremiya 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzapatsa nkhosazo abusa ndipo adzaziweta.+ Sizidzaopanso kanthu kapena kugwidwa ndi mantha aakulu,+ ndipo palibe imene idzasowa,” watero Yehova. Zefaniya 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Otsala mwa Isiraeli+ sadzachita zinthu zosalungama+ kapena kunena bodza.+ Sadzakhala ndi lilime lachinyengo+ koma iwo adzadya ndi kugona pansi momasuka+ ndipo sipadzakhala wowaopsa.”+
4 Adzakutchinjiriza ndi mapiko ake,+Udzathawira pansi pa mapiko ake.+Choonadi chake+ chidzakhala chishango chako+ chachikulu ndi malo ako achitetezo.
4 Ndidzapatsa nkhosazo abusa ndipo adzaziweta.+ Sizidzaopanso kanthu kapena kugwidwa ndi mantha aakulu,+ ndipo palibe imene idzasowa,” watero Yehova.
13 Otsala mwa Isiraeli+ sadzachita zinthu zosalungama+ kapena kunena bodza.+ Sadzakhala ndi lilime lachinyengo+ koma iwo adzadya ndi kugona pansi momasuka+ ndipo sipadzakhala wowaopsa.”+