2 Samueli 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhazikika pamaso pako mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+ Salimo 89:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndidzamusonyeza kukoma mtima kwanga kosatha mpaka kalekale,+Ndipo pangano limene ndinachita naye silidzaphwanyidwa.+ Yeremiya 33:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Yehova wanena kuti, ‘Monga momwedi ndinakhazikitsira pangano langa loti kukhale usana ndi usiku,+ malamulo anga akumwamba ndi dziko lapansi,+ Machitidwe 13:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndipo mfundo yakuti iye anamuukitsa kwa akufa, osayembekezera kubwereranso kuthupi limene lingathe kuvunda, anaitchula motere, ‘Ine ndidzakusonyezani anthu inu kukoma mtima kwanga kosatha ndi kokhulupirika, kumene ndinasonyeza Davide.’+
16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhazikika pamaso pako mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+
28 Ndidzamusonyeza kukoma mtima kwanga kosatha mpaka kalekale,+Ndipo pangano limene ndinachita naye silidzaphwanyidwa.+
25 “Yehova wanena kuti, ‘Monga momwedi ndinakhazikitsira pangano langa loti kukhale usana ndi usiku,+ malamulo anga akumwamba ndi dziko lapansi,+
34 Ndipo mfundo yakuti iye anamuukitsa kwa akufa, osayembekezera kubwereranso kuthupi limene lingathe kuvunda, anaitchula motere, ‘Ine ndidzakusonyezani anthu inu kukoma mtima kwanga kosatha ndi kokhulupirika, kumene ndinasonyeza Davide.’+