Yesaya 49:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako anandiuza kuti: “Iwe Isiraeli ndiwe mtumiki wanga.+ Ine ndidzaonetsera kukongola kwanga pa iwe.”+ Machitidwe 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzachita zimenezi kuti anthu otsalirawo afunefune Yehova ndi mtima wonse. Amufunefune pamodzi ndi mitundu yonse ya anthu, anthu otchedwa ndi dzina langa, watero Yehova amene akuchita zinthu zimenezi,+
3 Kenako anandiuza kuti: “Iwe Isiraeli ndiwe mtumiki wanga.+ Ine ndidzaonetsera kukongola kwanga pa iwe.”+
17 Ndidzachita zimenezi kuti anthu otsalirawo afunefune Yehova ndi mtima wonse. Amufunefune pamodzi ndi mitundu yonse ya anthu, anthu otchedwa ndi dzina langa, watero Yehova amene akuchita zinthu zimenezi,+