-
Ezekieli 32:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Bedi lake aliika pakati pa anthu ophedwa,+ aliika pakati pa khamu lake lonse. Manda a anthu ake azungulira bedilo. Onsewo ndi anthu osadulidwa, ophedwa ndi lupanga+ chifukwa anachititsa mantha anthu m’dziko la anthu amoyo. Adzanyozeka limodzi ndi amene akutsikira kudzenje. Iye waikidwa m’manda pakati pa anthu ophedwa.
-