Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kenako ndinauza mfumu kuti: “Ngati zili bwino ndi inu mfumu,+ ndipo ngati ine mtumiki wanu mungandikomere mtima,+ munditumize ku Yuda, kumzinda umene makolo anga anaikidwako kuti ndikaumangenso.”+

  • Yeremiya 31:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 “Taonani! Masiku adzafika,” watero Yehova, “pamene anthu adzamangira+ Yehova mzinda kuyambira pa Nsanja ya Hananeli+ mpaka ku Chipata cha Pakona.+

  • Amosi 9:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pamenepo ndidzasonkhanitsa ndi kubwezeretsa anthu anga Aisiraeli amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita ku ukapolo.+ Iwo adzamanga mizinda imene ili yabwinja ndi kukhalamo.+ Adzalima minda ya mpesa ndi kumwa vinyo wochokera m’mindayo. Adzalimanso minda ya zipatso ndi kudya zipatso zochokera m’mindayo.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena