Yesaya 61:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo adzamanganso malo amene akhala owonongeka kwa nthawi yaitali.+ Adzamanga malo amene anasakazidwa kalekale.+ Adzakonzanso mizinda yowonongedwa,+ malo amene akhala osakazidwa ku mibadwomibadwo. Yesaya 65:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo adzamanga nyumba n’kukhalamo.+ Adzabzala minda ya mpesa n’kudya zipatso zake.+ Ezekieli 36:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Pa tsiku limene ndidzakuyeretseni kuchotsa zolakwa zanu zonse, ndidzachititsanso kuti m’mizinda yanu mukhale anthu+ ndipo malo owonongeka adzamangidwanso.+
4 Iwo adzamanganso malo amene akhala owonongeka kwa nthawi yaitali.+ Adzamanga malo amene anasakazidwa kalekale.+ Adzakonzanso mizinda yowonongedwa,+ malo amene akhala osakazidwa ku mibadwomibadwo.
33 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Pa tsiku limene ndidzakuyeretseni kuchotsa zolakwa zanu zonse, ndidzachititsanso kuti m’mizinda yanu mukhale anthu+ ndipo malo owonongeka adzamangidwanso.+