Yesaya 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye adzameza imfa kwamuyaya+ ndipo Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzapukuta misozi pankhope zonse za anthu.+ Adzachotsa kunyozeka kwa anthu ake padziko lonse lapansi,+ pakuti Yehova ndiye wanena zimenezi. Mateyu 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Odala ndi anthu amene akumva chisoni, chifukwa adzasangalatsidwa.+ Luka 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Inu amene mukumva njala+ tsopano ndinu odala, chifukwa mudzakhuta.+ “Inu amene mukulira tsopano ndinu odala, chifukwa mudzaseka.+
8 Iye adzameza imfa kwamuyaya+ ndipo Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzapukuta misozi pankhope zonse za anthu.+ Adzachotsa kunyozeka kwa anthu ake padziko lonse lapansi,+ pakuti Yehova ndiye wanena zimenezi.
21 “Inu amene mukumva njala+ tsopano ndinu odala, chifukwa mudzakhuta.+ “Inu amene mukulira tsopano ndinu odala, chifukwa mudzaseka.+