Yesaya 34:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti Yehova ali ndi tsiku lobwezera adani ake,+ ndi chaka chopereka chilango, chifukwa cha zolakwa zimene Ziyoni anachitiridwa.+ Yesaya 35:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Amene ali ndi nkhawa mumtima mwawo muwauze kuti:+ “Limbani mtima.+ Musachite mantha.+ Pakuti Mulungu wanu adzabwera n’kudzabwezera adani anu.+ Mulungu adzabwezera chilango.+ Iye adzabwera n’kukupulumutsani.”+ Yesaya 61:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Wandituma kuti ndikalengeze za chaka cha Yehova chokomera anthu mtima,+ ndi za tsiku lobwezera la Mulungu wathu.+ Wanditumanso kuti ndikatonthoze anthu onse olira,+
8 Pakuti Yehova ali ndi tsiku lobwezera adani ake,+ ndi chaka chopereka chilango, chifukwa cha zolakwa zimene Ziyoni anachitiridwa.+
4 Amene ali ndi nkhawa mumtima mwawo muwauze kuti:+ “Limbani mtima.+ Musachite mantha.+ Pakuti Mulungu wanu adzabwera n’kudzabwezera adani anu.+ Mulungu adzabwezera chilango.+ Iye adzabwera n’kukupulumutsani.”+
2 Wandituma kuti ndikalengeze za chaka cha Yehova chokomera anthu mtima,+ ndi za tsiku lobwezera la Mulungu wathu.+ Wanditumanso kuti ndikatonthoze anthu onse olira,+