Salimo 59:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Afafanizeni mu mkwiyo wanu.+Afafanizeni kuti asakhaleponso.Ndipo adziwe kuti Mulungu akulamulira Yakobo mpaka kumalekezero a dziko lonse lapansi.+ [Seʹlah.] Yesaya 59:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye adzawapatsa mphoto mogwirizana ndi zochita zawo.+ Adani ake adzawapatsa mkwiyo ndipo anthu otsutsana naye adzawapatsa chilango chowayenerera.+ Zilumbanso adzazipatsa chilango choyenerera.+
13 Afafanizeni mu mkwiyo wanu.+Afafanizeni kuti asakhaleponso.Ndipo adziwe kuti Mulungu akulamulira Yakobo mpaka kumalekezero a dziko lonse lapansi.+ [Seʹlah.]
18 Iye adzawapatsa mphoto mogwirizana ndi zochita zawo.+ Adani ake adzawapatsa mkwiyo ndipo anthu otsutsana naye adzawapatsa chilango chowayenerera.+ Zilumbanso adzazipatsa chilango choyenerera.+