Salimo 78:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mulungu anachita zodabwitsa pamaso pa makolo awo+M’dziko la Iguputo,+ m’dera la Zowani.+ Salimo 105:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kumbukirani ntchito zodabwitsa zimene wachita,+Kumbukirani zozizwitsa zake ndi zigamulo zotuluka m’kamwa mwake,+
5 Kumbukirani ntchito zodabwitsa zimene wachita,+Kumbukirani zozizwitsa zake ndi zigamulo zotuluka m’kamwa mwake,+