Ekisodo 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno mngelo+ wa Mulungu woona amene anali kuyenda patsogolo pa Aisiraeli anachoka n’kupita kumbuyo kwawo. Motero, mtambo woima njo ngati chipilala uja unachoka kutsogolo n’kukaima kumbuyo kwawo.+ Ekisodo 23:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Tsopano ndikukutumizira mngelo+ wokutsogolera kuti akuteteze m’njira ndi kukakulowetsa m’dziko limene ndakukonzera.+
19 Ndiyeno mngelo+ wa Mulungu woona amene anali kuyenda patsogolo pa Aisiraeli anachoka n’kupita kumbuyo kwawo. Motero, mtambo woima njo ngati chipilala uja unachoka kutsogolo n’kukaima kumbuyo kwawo.+
20 “Tsopano ndikukutumizira mngelo+ wokutsogolera kuti akuteteze m’njira ndi kukakulowetsa m’dziko limene ndakukonzera.+