Ekisodo 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho ukamuuze Farao kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Isiraeli ndi mwana wanga wamwamuna, mwana wanga woyamba kubadwa.+ Deuteronomo 32:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kodi mukupitiriza kuchitira Yehova mwa njira imeneyi,+Anthu opusa ndi opanda nzeru inu?+Kodi iye si Atate wanu amene anakulengani,+Amene anakupangani ndi kukuchititsani kukhazikika?+ Yeremiya 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ine ndanena kuti, ‘Mokondwera ndinakuikani pakati pa ana anga ndi kukupatsani dziko labwino,+ cholowa chimene mitundu yambiri ya anthu imachisirira!’ Ndipo ndinanenanso kuti, ‘Anthu inu mudzandiitana kuti, “Atate wanga!”+ ndipo mudzandilondola osabwerera.’
22 Choncho ukamuuze Farao kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Isiraeli ndi mwana wanga wamwamuna, mwana wanga woyamba kubadwa.+
6 Kodi mukupitiriza kuchitira Yehova mwa njira imeneyi,+Anthu opusa ndi opanda nzeru inu?+Kodi iye si Atate wanu amene anakulengani,+Amene anakupangani ndi kukuchititsani kukhazikika?+
19 Ine ndanena kuti, ‘Mokondwera ndinakuikani pakati pa ana anga ndi kukupatsani dziko labwino,+ cholowa chimene mitundu yambiri ya anthu imachisirira!’ Ndipo ndinanenanso kuti, ‘Anthu inu mudzandiitana kuti, “Atate wanga!”+ ndipo mudzandilondola osabwerera.’