Salimo 74:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumbukirani anthu amene munawatenga kukhala anu kalelo,+Fuko limene munaliwombola monga cholowa chanu,+Ndi phiri la Ziyoni ili mmene inu mukukhala.+ Salimo 80:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu Mulungu wa makamu, chonde bwererani.+Yang’anani pansi pano muli kumwambako, ndipo onani ndi kusamalira mtengo wa mpesa uwu.+ Salimo 135:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ya wadzisankhira Yakobo,+Wadzisankhira Isiraeli kukhala chuma chake chapadera.+
2 Kumbukirani anthu amene munawatenga kukhala anu kalelo,+Fuko limene munaliwombola monga cholowa chanu,+Ndi phiri la Ziyoni ili mmene inu mukukhala.+
14 Inu Mulungu wa makamu, chonde bwererani.+Yang’anani pansi pano muli kumwambako, ndipo onani ndi kusamalira mtengo wa mpesa uwu.+ Salimo 135:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ya wadzisankhira Yakobo,+Wadzisankhira Isiraeli kukhala chuma chake chapadera.+