Deuteronomo 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu.+ Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, mwa anthu onse okhala padziko lapansi.+ Salimo 79:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ife, anthu anu, nkhosa zimene mukuweta,+Tidzakuyamikani mpaka kalekale.Tidzakutamandani ku mibadwomibadwo.+
6 Pakuti ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu.+ Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, mwa anthu onse okhala padziko lapansi.+
13 Koma ife, anthu anu, nkhosa zimene mukuweta,+Tidzakuyamikani mpaka kalekale.Tidzakutamandani ku mibadwomibadwo.+