Salimo 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 N’chifukwa chiyani inu Yehova mukuima kutali?+N’chifukwa chiyani mukubisala pa nthawi ya masautso?+ Salimo 74:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 N’chifukwa chiyani mwachotsa dzanja lanu, dzanja lanu lamanja,+Pachifuwa panu koma osachitapo kanthu? Kodi mukatero ife sitiwonongedwa? Zekariya 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho mngelo wa Yehova anati: “Inu Yehova wa makamu, kodi Yerusalemu ndi mizinda ya Yuda imene munaikana ndi kuisiya kwa zaka 70,+ simuichitira chifundo kufikira liti?”+
10 N’chifukwa chiyani inu Yehova mukuima kutali?+N’chifukwa chiyani mukubisala pa nthawi ya masautso?+
11 N’chifukwa chiyani mwachotsa dzanja lanu, dzanja lanu lamanja,+Pachifuwa panu koma osachitapo kanthu? Kodi mukatero ife sitiwonongedwa?
12 Choncho mngelo wa Yehova anati: “Inu Yehova wa makamu, kodi Yerusalemu ndi mizinda ya Yuda imene munaikana ndi kuisiya kwa zaka 70,+ simuichitira chifundo kufikira liti?”+