Salimo 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Umenewo ndiwo m’badwo wa amene amafunafuna Mulungu,M’badwo wa anthu ofunafuna nkhope yanu, inu Mulungu wa Yakobo.+ [Seʹlah.] Yesaya 55:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu inu funafunani Yehova pamene iye akupezekabe.+ Muitaneni akadali pafupi.+
6 Umenewo ndiwo m’badwo wa amene amafunafuna Mulungu,M’badwo wa anthu ofunafuna nkhope yanu, inu Mulungu wa Yakobo.+ [Seʹlah.]